Tsiku lililonse ndi mphatso yamtengo wapatali yochokera kwa Mulungu, yokhala ndi chisomo chatsopano ndi mwayi watsopano.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Choonadi cha mmene tiyenera kutumikira.
Kodi chochititsa chenicheni cha kusagwirizana konse ndi mikangano nchiyani?
Ndinadziŵa kuti sindinali kukhala ndi moyo monga wophunzira, kufikira pamene chokumana nacho chosintha moyo chinandikakamiza kuyandikira kwa Mulungu.
Ndani kapena n'chiyani chimasankha ngati ndidzakwiya ndi anthu amene ndimakhala nawo?
Kodi zimene mumachita monga Mkhristu Lolemba si funso lofunika kwambiri?
Kodi ndimakhala ndi moyo kwa ndani? Kodi ndikutumikira Mulungu kapena anthu?
Kodi n'chiyani chimachititsa kuti moyo wa wophunzira ukhale wapadera kwambiri?
Umboni wonena za kukhala ndi moyo wokondweretsa Mulungu.
Wodzikonda kapena mthandizi?
Monga mayi wotanganidwa, ndinali kuyesa kuchita zonse bwino, koma mpaka pamene ndinayambadi kufunafuna ufumu wa Mulungu choyamba ndi pamene zonse zinaonekeratu kwa ine.
Mmene ndinagonjetsera malingaliro amdima ndi olemera.
Mulungu akufuna kuti tifunefune chifuniro Chake m'zonse, kuphatikizapo mikhalidwe imene tili nayo tsopano, ndi m'zinthu zimene tili otanganitsidwa nazo tsopano.
Choonadi chodabwitsa ponena za mmene zimakhalira zovuta kukhala wabwino.
Kodi nthawi zina mumamva ngati zonse zikukutsutsani? Umu ndi mmene ndikumvera lero
Mmene chiwopsezo cha bomba chinayesera chidaliro changa mwa Mulungu.
Ndaphunzira kuti njira yokhala ndi anthu ovuta ndi kuphunzira kusamalira zochita zanga.
Aliyense amafuna mtendere wadziko lonse, koma kupangamtendere kumayamba ndi ine
M'pofunika kumvetsa kuti kuchimwa ndi kuyesedwa ku uchimo ndi zinthu ziwiri zosiyana.
Werengani mmene achinyamata ena amachitira zimenezi pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku
Nchifukwa chiyani mumalankhula zoterezo? Kodi mukudandaula kuti ena aganiza zotani za inu? Kodi mukufuna kumasulidwa?
Tonse tikudziwa kuti kuimba mlandu ena sikumathandiza konse munyengo yotere, komabe mchitidwe wotere uli mu mkhalidwe wathu wokonda kuchita zoipa kuyambira pachiyambi …
Zingakhale zovuta kupeza tanthauzo la moyo pamene tsiku lililonse likungodutsa mofanana ndi kale, kufikira mutayamba kuyang'ana moyo m'njira yatsopano kotheratu.
Kuimba mlandu ena n'kwachibadwa mofanana ndi kupuma kwa anthu ambiri.