Mmene timaganizira ndi kuchitira ndi anthu osoŵa, osauka ndi amene dziko limawayang'ana pansi, zimasonyeza zimene timaganiza ponena za Mulungu, Mlengi.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Choonadi chodabwitsa ponena za mmene zimakhalira zovuta kukhala wabwino.
Ndaphunzira kuti njira yokhala ndi anthu ovuta ndi kuphunzira kusamalira zochita zanga.
Nkhani ya Mariya ndi Elizabeti m'Baibulo imafotokoza za ubwenzi wabwino kwambiri. Kodi n'chiyani chinapangitsa ubwenzi wawo kukhala wolimba kwambiri?
Pali chiweruzo chomwe chiri chothandizira, ndipo pali chiweruzo chomwe chiri choipa ndi chovulaza. Chimodzi ndi kuwala ndipo chimodzi ndi mdima. Werengani zambiri apa!
Filimu ina m'kalasi ya Chingelezi inandipangitsa kuganizira zimene mawu anga okhudza kwambiri anthu amene ndili nawo.
Nchifukwa chiyani mumalankhula zoterezo? Kodi mukudandaula kuti ena aganiza zotani za inu? Kodi mukufuna kumasulidwa?
Tonse tikudziwa kuti kuimba mlandu ena sikumathandiza konse munyengo yotere, komabe mchitidwe wotere uli mu mkhalidwe wathu wokonda kuchita zoipa kuyambira pachiyambi …
Kodi zolinga ndi zotsatira za chikondi changa n'zotani? Kodi ndili ndi chikondi chomwe chimangoganizira za ine ndekha kapena chikondi chopatsa moyo, chopanda dyera?