Mndandanda wa zinthu zimene sindingathe kuchita ndi wosatha. Koma ndikhoza kuchita mbali yaing'ono yomwe ili patsogolo panga.
Kodi mungamve bwanji kudziwa kuti moyo wanu wakhala wopanda pake?
Pafupifupi Akristu onse amayang'ana chimene chiri chachikulu, ndipo amafuna kuti ana awo akhale aakulu m'dziko. Koma zimenezi si zimene Mulungu amafuna kwa ife!
Ndinadziŵa kuti sindinali kukhala ndi moyo monga wophunzira, kufikira pamene chokumana nacho chosintha moyo chinandikakamiza kuyandikira kwa Mulungu.
Baibulo limanena za kudzinyenga nokha, ndipo zimenezi zingachitike mosavuta kuposa mmene mukuganizira. Koma palinso njira yosavuta yopeŵera.
Moyo wanga unasintha nditazindikira kuti kupereka n'kwabwino kwambiri kuposa kulandira.
Awa ndi mavesi angapo onena za lonjezo laulemerero la Mulungu kwa ife: tingagonjetse uchimo!
Pali kusiyana kwakukulu. Ndipo n'kofunika kwambiri kudziwa kusiyana kwake.
Nkhondo ya Mayi wina pa kudziyerekeza ndi ena.
Kodi ndikugwiritsa ntchito bwanji mwayi umenewu?
Kukhala Mkristu n'kwabwino kwambiri kuposa mmene tingaganizire.
Machimo ambiri amagwirizana mwachindunji ndi mfundo zitatu zazikuluzi.
Ife tonse tili ndi zilakolako zoipa mu thupi lathu zimene zimatichititsa kuchita uchimo. Kodi tingapulumutsidwe bwanji ku vuto limeneli?