Ndikamayenda m'kuunika, moyo umakhala wabwino, ndipo nthawi zonse ndimakhala ndi chikumbumtima chabwino. Koma kodi ndimayenda bwanji m'kuunika?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Timawerenga zambiri zokhudza mtima wa m'Baibulo. Koma kodi mtima wathu kwenikweni nchiyani, kunena mwauzimu? Kodi mtima wathu uli ndi kufunika kotani?
Kodi munayamba mwakayikirapo kuti Mulungu amakukondani? Mavesi a m'Baibulo amenewa angasinthe zimenezo.
Pokhala ndi "chidziwitso" chochuluka chomwe chilipo ndipo aliyense akuyesera kutiuza kuti akunena zoona, kodi n'zotheka bwanji kudziwa zomwe zilidi zoona?
M'Baibulo, Yesu wapatsidwa mayina osiyanasiyana. Kodi munayamba mwaganizapo za zimene ena mwa mayina ndi maudindo amenewa amatanthauza kwa ife patokha?
Kukhulupirira si kungovomereza kuti Baibulo ndi loona.