Zochitika zake zatsimikizira kuti moyo uno ndi weniweni.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Njira ya moyo wanga imapangidwa ndi zosankha za tsiku ndi tsiku zomwe ndimapanga.
Pamene ndilingalira za chiitano changa monga Mkristu, kodi ndili ndi chidwi chotani m'kuchikwaniritsa?
Kusangalala ndi anthu amene ali osangalala n'kosavuta kunena kuposa kuchita. Koma ngati ndingaphunzire momwe ndingachitire zimenezo - tangoganizani momwe ndidzasangalala kwambiri!
Kodi ndingasunge bwanji moyo wanga woganiza kukhala woyera pamene ambiri mwa malingaliro awa angobwera popanda ine kuwafuna?
Ndingaone kuti ndimakhala wodetsedwa ndikayesedwa. Koma kodi ndinachimwa?
Kodi Baibulo limatanthauza chiyani likanena kuti tiyenera kukhala "oposa ogonjetsa?" Kodi limalankhula za ndani pamene linalembedwa "kwa iye amene agonjetsa?"
Kodi tiyenera kugonjetsa chiyani? N'chifukwa chiyani zili zoipa kwambiri?
Kodi Mzimu Woyera ndani? N'chifukwa chiyani ndimamufuna?
Si chinthu choipa kudziwa kufooka kwanu pankhani ya uchimo. Ayi, ayi! Koma kodi mukudziwa kumene mungapeze mphamvu?
M'pofunika kumvetsa kuti kuchimwa ndi kuyesedwa ku uchimo ndi zinthu ziwiri zosiyana.
Pali nkhondo yoti timenye, nkhondo yolimbana ndi uchimo, umene ulu muzu wa mazunzo onse.
Sitifunikira kudziimba mlandu pamene tikuyesedwa. Pano pali chifukwa chake ...