Pamene mzimu wa chikhulupiriro unalowa mumtima mwanga, maganizo anga pa moyo asintha n'kuyamba kuwona zinthu moyenera
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Poyamba kudzipatula ndi kulumikizana pa intaneti kunali chinthu chatsopano komanso chosangalatsa - mpaka ndinazindikira kuti magwero athu a ndalama akuchepetsedwa mmodzi ndi mmodzi.
Kodi tingapeze bwanji tchalitchi choyenera pakati pa anthu ambiri chonchi?
Internet, mafoni ndi chirichonse chimene chimabwera nawo – kodi Mkhristu ayenera kuchita bwanji ndi zinthu zonsezi?
N'chifukwa chiyani nthawi zonse mumakhala woyamikira komanso wosangalala, mosasamala kanthu za mmene zinthu zilili pa moyo wanu kapena mmene mukumvera.
Kodi munayamba mwaganizapo kapena kunena mawu amenewa? Kodi mukudziwa zimene Mulungu anauza Yeremiya pamene ananena zimenezi?
Tiyeni tiyambe chaka chatsopano chodzaza ndi chiyembekezo ndi chikhulupiriro chamoyo m'mawu onse a Mulungu.
Kodi ndikuchita zinthu zofanana ndi zimene ndimadzudzula ena?
Kodi munthu aliyense angasankhe bwanji kuti moyo wina wa munthu ndi wopanda mtengo kuposa wawo?
Mu kukhumudwa kwanga ndi mkwiyo wanga za dziko limene ndimakhala, ndinapeza vumbulutso lofunika: kwenikweni ndi udindo wanga kupempherera dziko langa.
Vesi ili lili ngati mgwirizano pakati pa ine ndi Mulungu: "Mulungu amatsutsana ndi onyada, koma Iye amapereka chisomo kwa odzichepetsa.".
Imfa m'banja inandipangitsa kuganiza ...
Kodi n'chiyani chimatichititsa kuchita ntchito zabwino zimene timachita?
Pokhala ndi "chidziwitso" chochuluka chomwe chilipo ndipo aliyense akuyesera kutiuza kuti akunena zoona, kodi n'zotheka bwanji kudziwa zomwe zilidi zoona?
Estere anali "msilikali wa pemphero", mkazi woopa Mulungu wokhala ndi mgwirizano wolimba waumwini ndi Yesu.
Wodzikonda kapena mthandizi?
Sukulu zina zimakhala ndi masiku "owonetsera ndi kuuza". Ndinaganiza za momwe zimenezo zimagwiriranso ntchito pamene tikufuna kugawana uthenga wabwino ndi ena ..
Nkhani ya Mariya ndi Elizabeti m'Baibulo imafotokoza za ubwenzi wabwino kwambiri. Kodi n'chiyani chinapangitsa ubwenzi wawo kukhala wolimba kwambiri?
Aliyense amafuna mtendere wadziko lonse, koma kupangamtendere kumayamba ndi ine
Tonse tikudziwa kuti kuimba mlandu ena sikumathandiza konse munyengo yotere, komabe mchitidwe wotere uli mu mkhalidwe wathu wokonda kuchita zoipa kuyambira pachiyambi …
Chikwangwani chimene ndinaona popita kuntchito chinandichititsa kuganizira za Khirisimasi yoyamba ku Betelehemu.
Kutsatira maphunziro atatu ameneŵa kudzakuthandizani kukhala ndi maunansi abwino, odalitsika, athanzi!
Kuimba mlandu ena n'kwachibadwa mofanana ndi kupuma kwa anthu ambiri.