Chifuniro cha Mulungu m'ntchito yathu ya padziko lapansi
Mulungu akufuna kuti tifunefune chifuniro Chake m'zonse, kuphatikizapo mikhalidwe imene tili nayo tsopano, ndi m'zinthu zimene tili otanganitsidwa nazo tsopano.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita