Iyi ndi nkhani yanga - nkhani ya chikhulupiriro.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Nthawi zina "maluso" angatanthauze chinthu chosiyana kwambiri ndi zimene mungaganize.
Mmene ndinagonjetsera malingaliro amdima ndi olemera.
Monga mayi wotanganidwa, ndinali kuyesa kuchita zonse bwino, koma mpaka pamene ndinayambadi kufunafuna ufumu wa Mulungu choyamba ndi pamene zonse zinaonekeratu kwa ine.
Ndaphunzira kuti njira yokhala ndi anthu ovuta ndi kuphunzira kusamalira zochita zanga.
Choonadi chodabwitsa ponena za mmene zimakhalira zovuta kukhala wabwino.
Ngakhale kuti Anelle wakhala akukhala ndi matenda kwa zaka zambiri, iye ndi mtsikana amene waphunzira kukhala wokhutira kwambiri.
Kodi zingatheke bwanji kuti tisamade nkhawa ndi chilichonse m’dziko limene zinthu zambiri n’zosatsimikizika?