Kodi tikudziwa bwanji kuti Mulungu amatikonda? Chofunika kwambiri: Kodi Mulungu amadziwa bwanji kuti timamukonda?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Nkhani ya mayi ya zomwe anakumana nazo pamene analola maloto ake a moyo "wangwiro".
Kuti mupeze mtendere wa Mulungu umene udzasunga mtima ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu, muyenera kumenyana!
Kukhulupirira Mulungu ndiko kukhulupirira kuti Iye alipo ndi kuti Mawu Ake ndi oona. Ndipo ngati timakhulupirira izi, ziyenera kukhala ndi zotsatira zazikulu pa moyo wathu wa tsiku ndi tsiku ...
Ndinadziŵa kuti sindinali kukhala ndi moyo monga wophunzira, kufikira pamene chokumana nacho chosintha moyo chinandikakamiza kuyandikira kwa Mulungu.
Choonadi cha mmene tiyenera kutumikira.
Linda anapeza ufulu weniweni pamene anazindikira kuti panali Mmodzi yekha amene anayenera kumukondweretsa.
Nthawi zina "maluso" angatanthauze chinthu chosiyana kwambiri ndi zimene mungaganize.
Estere anali "msilikali wa pemphero", mkazi woopa Mulungu wokhala ndi mgwirizano wolimba waumwini ndi Yesu.
Kodi munayamba mwakayikirapo kuti Mulungu amakukondani? Mavesi a m'Baibulo amenewa angasinthe zimenezo.
Umboni wonena za kukhala ndi moyo wokondweretsa Mulungu.
Mulungu akufuna kuti tifunefune chifuniro Chake m'zonse, kuphatikizapo mikhalidwe imene tili nayo tsopano, ndi m'zinthu zimene tili otanganitsidwa nazo tsopano.
Kodi mumakhulupirira zozizwitsa? Kodi chozizwitsa chimaoneka bwanji kwa inu?
Mmene timaganizira ndi kuchitira ndi anthu osoŵa, osauka ndi amene dziko limawayang'ana pansi, zimasonyeza zimene timaganiza ponena za Mulungu, Mlengi.
Mulungu akufuna kukhala ndi mzimu wathu, ndipo Iye akufuna kupanga nyumba Yake mwa ife kachiwiri. Kodi Iye amachita bwanji zimenezi?
Werengani mmene achinyamata ena amachitira zimenezi pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku
Pali chiweruzo chomwe chiri chothandizira, ndipo pali chiweruzo chomwe chiri choipa ndi chovulaza. Chimodzi ndi kuwala ndipo chimodzi ndi mdima. Werengani zambiri apa!
Kodi tikudziwa kuti nthawi zonse Mulungu ali pafupi kwambiri ndi ife? Tsiku lili lonse, m'moyo wathu wonse?
Ukada nkhawa, umamupangitsa Mulungu kukhala wamng’ono komanso kuti iweyo ukhale wamkulu. Kunena zoona mukunena kuti Mulungu ndi wabodza.
Samueli anali wopatulika kuyambira umwana wake wonse. Moyo wake umatiwonetsa ubwino omvetsera mawu a Mulungu ndi kuwamvera ,nthawi zonse.