Nkhondo ya Mayi wina pa kudziyerekeza ndi ena.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
N'zosakayikitsa kuti Mulungu amaona kuti ukwati ndi ubale wopatulika.
Kodi nyumba yanu ndi chidutswa chakumwamba cha ana anu?
Njira yopapatiza ndiyo njira ya moyo. Zimatanthauza kusiya chinachake - koma zotsatira zake ndizodabwitsa!
Akristu ambiri akukambirana ngati anthu osudzulidwa angakwatirenso kapena ayi. Koma kodi Mawu a Mulungu amati chiyani?
Rolf: Anthu ena amakwiya msanga. Ndine mmodzi wa iwo.
Umboni woona mtima wa mayi wa mmene ndemanga yosavuta ya mwana wake inamusonyezera choonadi ponena za iye mwini.
"Pemphero ndi limodzi mwa mizati yaikulu m'moyo wanga. Ndine wokondwa kwambiri kuti ndikhoza kupita kwa Mulungu ndi kupeza thandizo. Kumbi ndingachita wuli asani ndisoŵa?"
Chiyero ndi chinthu chomwe chikukhala chachilendo kwambiri.
Monga mayi wotanganidwa, ndinali kuyesa kuchita zonse bwino, koma mpaka pamene ndinayambadi kufunafuna ufumu wa Mulungu choyamba ndi pamene zonse zinaonekeratu kwa ine.