Kukayikira koipa n'kosiyana kotheratu ndi chitsanzo chosiyidwa ndi Kristu, ndipo kumachokera ku kusoŵeka kwa chikondi. Koma pali njira yotulukira m'malingaliro oipa ameneŵa!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Chilichonse chimene timanena chimachokera ku malingaliro athu.
Filimu ina m'kalasi ya Chingelezi inandipangitsa kuganizira zimene mawu anga okhudza kwambiri anthu amene ndili nawo.