Kodi kukhulupirira Mulungu kumatanthauzanji?
Kukhulupirira Mulungu ndiko kukhulupirira kuti Iye alipo ndi kuti Mawu Ake ndi oona. Ndipo ngati timakhulupirira izi, ziyenera kukhala ndi zotsatira zazikulu pa moyo wathu wa tsiku ndi tsiku ...
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita