Nkhani ya Mariya ndi Elizabeti m'Baibulo imafotokoza za ubwenzi wabwino kwambiri. Kodi n'chiyani chinapangitsa ubwenzi wawo kukhala wolimba kwambiri?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kodi zolinga ndi zotsatira za chikondi changa n'zotani? Kodi ndili ndi chikondi chomwe chimangoganizira za ine ndekha kapena chikondi chopatsa moyo, chopanda dyera?