Kukayikira koipa n'kosiyana kotheratu ndi chitsanzo chosiyidwa ndi Kristu, ndipo kumachokera ku kusoŵeka kwa chikondi. Koma pali njira yotulukira m'malingaliro oipa ameneŵa!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Chilichonse chimene timanena chimachokera ku malingaliro athu.
Kodi mukuchita chinachake mwachangu kuti musiye kuchimwa?
Njira ya moyo wanga imapangidwa ndi zosankha za tsiku ndi tsiku zomwe ndimapanga.
Kodi ndingasunge bwanji moyo wanga woganiza kukhala woyera pamene ambiri mwa malingaliro awa angobwera popanda ine kuwafuna?
"Maganizo anu ndi aulere," iwo akutero. Koma kodi zilidi? Kodi mumakhala ndi ufulu weniweni m'moyo wanu woganiza?