Kodi n'zotheka kudziwa Mulungu payekha?
Zikanatha kupita mosiyana kwambiri chifukwa cha "wolamulira wachinyamata wolemera" akanasankha kusiya zonse chifukwa cha Yesu.
Pokhala ndi "chidziwitso" chochuluka chomwe chilipo ndipo aliyense akuyesera kutiuza kuti akunena zoona, kodi n'zotheka bwanji kudziwa zomwe zilidi zoona?
Yesu ankatha kuona mmene Natanayeli analili asanalankhule ndi Iye. Kodi n'chiyani chinali chapadera kwambiri pa Natanayeli?
Chikwangwani chimene ndinaona popita kuntchito chinandichititsa kuganizira za Khirisimasi yoyamba ku Betelehemu.
Samueli anali wopatulika kuyambira umwana wake wonse. Moyo wake umatiwonetsa ubwino omvetsera mawu a Mulungu ndi kuwamvera ,nthawi zonse.