Mawu ndi amphamvu kwambiri. Amatha kumanga kapena kuphwanya, kulimbikitsa kapena kuwononga.
Kodi mungamve bwanji ngati muli ndi amuna 300 okha amene mungalimbane ndi gulu lankhondo lalikulu?
Lamulo la Mulungu ndi losavuta komanso lomveka bwino: "Uskakhala ndi mulungu wina aliyense koma ine." Eksodo 20:3
Ndani kapena n'chiyani chimasankha ngati ndidzakwiya ndi anthu amene ndimakhala nawo?
Kodi ndingatsimikizire bwanji kuti ndikugwiritsa ntchito luso langa kwa Mulungu?