Ndizodabwitsa zomwe zingachitike kudzera mu mphamvu ya mtanda!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Moyo wabwino kwambiri womwe ungakhale ndi aliyense, kulikonse, nthawi iliyonse. Ngati mukufunadi.
Kodi kupachikidwa ndi nsembe za Yesu zinali zosiyana bwanji ndi nsembe ndi chikhululukiro m'Pangano Lakale?
Amuna atatu anapachikidwa pamodzi pa Calvary, koma tsikulo linatha ndi zotsatira zitatu zosiyana kwambiri. Kodi chitsanzo chanu ndani?
Yesu ananena kuti mukhale wophunzira Wake, muyenera "kusenza mtanda wanu tsiku ndi tsiku". Kodi mungachite bwanji zimenezi?
Ichi ndi mfungulo yogonjetsera uchimo m'moyo wathu!
Kodi Yakobo anganene bwanji kuti tiyenera kukhala "odzala ndi chimwemwe" m'mayesero athu? Kodi kuvutika kungakhale kosangalatsa motani?
"Ngakhale mutakhala kuti kapena muli ndani, mukhoza kukhala wosangalala kwambiri."
Fedora akufotokoza mmene anakhalira womasuka kotheratu ku mkwiyo wake woipa.
Kodi tsogolo lingakhale bwanji labwino komanso lowala pamene nkhani zonse zili zoipa kwambiri?
Sitiyenera kulola Satana kuvutisa zinthu
Kutsatira maphunziro atatu ameneŵa kudzakuthandizani kukhala ndi maunansi abwino, odalitsika, athanzi!
Mmene Chikhristu choona chimaonekeradi.