Enoki analandira umboni wakuti anakondweretsa Mulungu.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Phunziro la kuimilira m'chikhulupiriro, kuchokera kwa mwana wamasiye amene anakhala mfumukazi.
Kodi mungatani mukazingidwa ndi adani anu?
Uthenga wa chiyembekezo kwa aliyense amene akuona ngati sali abwino mokwanira.
Tikakhala ndi mzimu wa chikhulupiriro, Mulungu angatithandize kugonjetsa zinthu zimene zingaoneke ngati zosatheka.
Msewu wopita ku Damasiko unali chiyambi chabe kwa Paulo.
N'chifukwa chiyani Mose anakhala mtsogoleri wamkulu chonchi?
Werengani nkhani yosonkhezera imeneyi yonena za kukhulupirika kwenikweni kwa Danieli, ndi chikhulupiriro chake mwa Mulungu zivute zitani.
Tingaphunzire zambiri pa nkhani ya Yosefe.
Kodi mungamve bwanji ngati muli ndi amuna 300 okha amene mungalimbane ndi gulu lankhondo lalikulu?
Kodi kupambana kwa Davide pa Goliati kungakhale chitsanzo chotani kwa ife masiku ano?
Zikanakhala zachibadwa kwathunthu kuti Sarah asakhulupirire kuti adzakhala ndi mwana wamwamuna ... pambuyo pake, anali ndi zaka 90.
Debora anali mneneri wamkazi ndi woweruza mu Israyeli. Iye ali chitsanzo champhamvu cha mmene chikhulupiriro m'zochita chimagwirira ntchito!
Yesu ankatha kuona mmene Natanayeli analili asanalankhule ndi Iye. Kodi n'chiyani chinali chapadera kwambiri pa Natanayeli?
Iye anali chabe mtsikana wabwinobwino wa ku Nazarete, koma anakhala mayi wa Yesu Kristu. Chifukwa chiyani iye?
Nkhani ya Mariya ndi Elizabeti m'Baibulo imafotokoza za ubwenzi wabwino kwambiri. Kodi n'chiyani chinapangitsa ubwenzi wawo kukhala wolimba kwambiri?
Samueli anali wopatulika kuyambira umwana wake wonse. Moyo wake umatiwonetsa ubwino omvetsera mawu a Mulungu ndi kuwamvera ,nthawi zonse.