Ngakhale kuti Anelle wakhala akukhala ndi matenda kwa zaka zambiri, iye ndi mtsikana amene waphunzira kukhala wokhutira kwambiri.