Kodi mukuona kuti mukuchitabe zinthu zoipa, ngakhale kuti mukufunadi kuchita zabwino?
Kodi n'zotheka kukhala ndi mzimu wofatsa komanso wabata pamene muli ndi umunthu wofuula komanso wamphamvu?
Tikudziwa kuti Baibulo limanena kuti Mulungu amatikonda. Koma kodi Iye ali kuti m'nthaŵi zovuta?