"Kodi ndimapita kuti kuchokera pano?" linali funso lomwe linali kuyaka mumtima mwa mnyamata wina wa ku Cameroon atatembenuzidwa.
Pali nkhondo yoti timenye, nkhondo yolimbana ndi uchimo, umene ulu muzu wa mazunzo onse.