Kuona anthu monga mmene Mulungu amawaonera, kumatithandiza pamene tili ndi zochita ndi anthu amphamvu, olamulira.