Baibulo limatiuza kuti machimo athu onse angakhululukidwe. Koma kodi zimenezi n'zothekadi?
Kodi mwawerengera mtengo wake?
Mothandizidwa ndi uthenga wabwino n'zotheka kukhala wopanda zolaula kwathunthu.