Ndinali nditazolowera kuvomereza mabodza ake, mpaka Mulungu anandisonyeza zimene zinafunika kusintha pa moyo wanga.