Kodi Yesu angatilamule bwanji kuti tizikonda anthu? Kodi mungatani kuti muzikonda munthu wina?
Pangakhale zifukwa zambiri za "kuchita chinthu choyenera". Kodi chifukwa chanu n'chiyani?
Kuimba mlandu ena n'kwachibadwa mofanana ndi kupuma kwa anthu ambiri.