Alta anakhumudwa mosavuta ndi aliyense ndi chirichonse ndipo izi zinali kuwononga moyo wake. Kodi angapeze bwanji njira yosiya kukhumudwa?