N'kutheka kuti n'zovuta kuona cholinga chachikulu mukapita kumalo amodzimodziwo masiku asanu pa mlungu!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Nchifukwa chiyani mumalankhula zoterezo? Kodi mukudandaula kuti ena aganiza zotani za inu? Kodi mukufuna kumasulidwa?