Satana akamagwira ntchito pakati pa anthu a Mulungu, amagwiritsa ntchito zilakolako zawo zachibadwa ndi zinthu zimene zimawakopa.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kumveka kwina pa nkhani yosangalatsa yomwe nthawi zambiri imamvedwa molakwika.
Mmene mungagonjetsere mabodza ndi zinenezo za Satana.
Ndinali nditazolowera kuvomereza mabodza ake, mpaka Mulungu anandisonyeza zimene zinafunika kusintha pa moyo wanga.
Cholinga cha Satana ndicho kutilekanitsa ndi Mulungu. Umu ndi mmene tingamuletsere.