Mmene mungagonjetsere mabodza ndi zinenezo za Satana.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Ndinali nditazolowera kuvomereza mabodza ake, mpaka Mulungu anandisonyeza zimene zinafunika kusintha pa moyo wanga.
Cholinga cha Satana ndicho kutilekanitsa ndi Mulungu. Umu ndi mmene tingamuletsere.