Kodi kupulumutsidwa kotheratu kumatanthauzanji?
Kupulumutsidwa kotheratu kumatanthauza kukhala ndi chipulumutso chakuya kwambiri; kupulumutsidwa osati kokha ku zotulukapo za uchimo, komanso ku unyolo weniweni wa uchimo.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita