Lonjezo lalikulu kwambiri limene Mulungu watipatsa n'lakuti tingasinthe kotheratu!
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Mulungu amafuna kutsogolera mzimu wathu ku mtendere ndi mpumulo. Kodi tidzamulola Iye kuchita izo?
Baibulo limanena za kugonjetsa uchimo. Anthu ambiri amabwera kwa Yesu kuti akhululukidwe machimo awo – koma bwanji kugonjetsa machimo amenewa?
Kugawana mu chikhalidwe chauMulungu kumatanthauza kuti chikhalidwe changa chimakhala ngati chikhalidwe cha Mulungu - kudzera mu ntchito Yake yolenga mwa ine!
Kupulumutsidwa kotheratu kumatanthauza kukhala ndi chipulumutso chakuya kwambiri; kupulumutsidwa osati kokha ku zotulukapo za uchimo, komanso ku unyolo weniweni wa uchimo.
Baibulo limanena za kukhala wangwiro. Kodi zimenezi zikutanthauzanji, ndipo kodi n'zotheka?
Kodi mukuchita chinachake mwachangu kuti musiye kuchimwa?
Kodi n'chiyani chimachititsa kuti moyo wa wophunzira ukhale wapadera kwambiri?
Fedora akufotokoza mmene anakhalira womasuka kotheratu ku mkwiyo wake woipa.
Pali chinthu chimodzi chokha chimene chingakupangitseni kukhala wosangalala ndi kukupatsani mpumulo.