"Kodi tsogolo lanu likuoneka bwanji? Kodi mwakonza moyo wanu?" Ndinayenera kuima ndi kuganiza ndisanayankhe.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Pamene chiyembekezo chathu chili mwa Kristu, tili ndi chiyembekezo cha mtsogolo mu ulemerero waukulu ndi wosatha.
Ndi Mulungu Mwini amene akulamulira malire a miyoyo yathu ndi cholinga chotikokera pafupi ndi Iyemwini.
Kodi mukufunadi kupeza chifuniro cha Mulungu m'moyo wanu wa tsiku ndi tsiku? Chofunika kwambiri ndi kusiya chifuniro chanu n'cholinga choti mupeze chifuniro cha Mulungu
Pafupifupi Akristu onse amayang'ana chimene chiri chachikulu, ndipo amafuna kuti ana awo akhale aakulu m'dziko. Koma zimenezi si zimene Mulungu amafuna kwa ife!
Ndapeza zifukwa zitatu zimene ndingayang'ane kutsogolo ndi kuyamikira chaka chikubwerachi ndi nthaŵi zimene zikubwera!
Kodi maganizo anu ali kuti m'moyo?
Kodi ndimachita chiyani ndikaona ngati sindine zonse zomwe ndiyenera kukhala?.
Pali njira imodzi yomwe sinakhumudwitsepo aliyense amene wasankha. Kodi mukuganiza kuti kutsatira maloto anu ndi njira imeneyo? Kapena pali zina?
Monga Akristu, kodi tingayembekezere chiyani m'chaka chatsopano?
Kodi tsogolo lingakhale bwanji labwino komanso lowala pamene nkhani zonse zili zoipa kwambiri?
Uthenga wabwino ndi woyembekezera chaka chotsatira.
Zingakhale zovuta kupeza tanthauzo la moyo pamene tsiku lililonse likungodutsa mofanana ndi kale, kufikira mutayamba kuyang'ana moyo m'njira yatsopano kotheratu.