Mulungu ankafuna kuti tikhale ndi moyo, koma pa chifukwa chotani?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Ndife anthu osankhidwa a Mulungu, osankhidwa Iye asanapange dziko. Kodi mumakhulupirira? Kodi mukukhala nazo?
Kodi anthufe tingatsatire bwanji Khristu, Mwana wa Mulungu?
Kodi muli ndi chiyembekezo cha moyo wosatha? Kodi mungakhale ndi moyo umene umatsogolera ku moyo wosatha m'nthaŵi yanu pano padziko lapansi?
Pafupifupi Akristu onse amayang'ana chimene chiri chachikulu, ndipo amafuna kuti ana awo akhale aakulu m'dziko. Koma zimenezi si zimene Mulungu amafuna kwa ife!
Monga Akristu tili ndi chiitano chapamwamba kwambiri ndi chopatulika, ndipo chimenecho sichidalira konse pa maphunziro athu kapena chiyambi kapena fuko!
Baibulo limanena za kukhala wangwiro. Kodi zimenezi zikutanthauzanji, ndipo kodi n'zotheka?
Pali njira imodzi yomwe sinakhumudwitsepo aliyense amene wasankha. Kodi mukuganiza kuti kutsatira maloto anu ndi njira imeneyo? Kapena pali zina?
Imfa m'banja inandipangitsa kuganiza ...
Pamene ndilingalira za chiitano changa monga Mkristu, kodi ndili ndi chidwi chotani m'kuchikwaniritsa?
Timaitanidwa kuti tikhale ana a Mulungu. Koma kodi tiyenera kutchedwa ana a Mulungu chiyani?
Mmene Chikhristu choona chimaonekeradi.