Mwina pali chinthu chimodzi chomwe simunachitenge mwamphamvu mokwanira ...
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kunyada ndi tchimo limene limakhudza munthu aliyense.
Kukhala ngati Mwana wa Mulungu kumadalira chinthu chimodzi chofunika kwambiri chimenechi.
Julia ataona kuti anali wonyada komanso wodzikuza, ankadziwa kuti pali chinachake chimene angachite.
Vesi ili lili ngati mgwirizano pakati pa ine ndi Mulungu: "Mulungu amatsutsana ndi onyada, koma Iye amapereka chisomo kwa odzichepetsa.".
Timanyadira kwambiri zomwe sitikuziwona n'komwe. Koma Mulungu akufuna kutimasula ku zimenezo!
Kodi ndingatsimikizire bwanji kuti ndikugwiritsa ntchito luso langa kwa Mulungu?