Monga Akristu, kodi tingayembekezere chiyani m'chaka chatsopano?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Nyengo ya Khirisimasi ingakhale yotanganidwa kwambiri moti tingaiwale mosavuta zimene tikukondwerera.
Uthenga wabwino ndi woyembekezera chaka chotsatira.
Pa Khirisimasi timaganiza za Mpulumutsi wathu. Koma kodi zimenezo zikutanthauzanji kwa ife?
Kodi tikudziwa kuti nthawi zonse Mulungu ali pafupi kwambiri ndi ife? Tsiku lili lonse, m'moyo wathu wonse?
Chaka chathachi sichinali chophweka, koma ndili ndi zifukwa zonse zokhalira ndi chikhulupiriro chamtsogolo
Chikwangwani chimene ndinaona popita kuntchito chinandichititsa kuganizira za Khirisimasi yoyamba ku Betelehemu.
Muziyamika mu nyengo zonse." Kodi tingachite bwanji zimenezi?