Umboni woona mtima wa mayi wa mmene ndemanga yosavuta ya mwana wake inamusonyezera choonadi ponena za iye mwini.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
"Pemphero ndi limodzi mwa mizati yaikulu m'moyo wanga. Ndine wokondwa kwambiri kuti ndikhoza kupita kwa Mulungu ndi kupeza thandizo. Kumbi ndingachita wuli asani ndisoŵa?"
Chiyero ndi chinthu chomwe chikukhala chachilendo kwambiri.
Monga mayi wotanganidwa, ndinali kuyesa kuchita zonse bwino, koma mpaka pamene ndinayambadi kufunafuna ufumu wa Mulungu choyamba ndi pamene zonse zinaonekeratu kwa ine.