Sindikusangalala kwambiri ndi mphatso, nyimbo ndi zokongoletsera zonse za nthawi ya Khirisimasi. Koma pali chinthu chimodzi chimene ndimasangalala nacho pa Khirisimasi.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Pamene Yesu anabadwa chiyembekezo chatsopano chinadza kwa aliyense amene anatopa ndi kukhala kapolo wa uchimo.
Iye anali chabe mtsikana wabwinobwino wa ku Nazarete, koma anakhala mayi wa Yesu Kristu. Chifukwa chiyani iye?
Nkhani ya Mariya ndi Elizabeti m'Baibulo imafotokoza za ubwenzi wabwino kwambiri. Kodi n'chiyani chinapangitsa ubwenzi wawo kukhala wolimba kwambiri?
Chimwemwe chachikulu chimenechi chimene angelo analankhula kalekale chinasintha zonse, ndipo chingasinthebe miyoyo yathu lero lino.
Nyengo ya Khirisimasi ingakhale yotanganidwa kwambiri moti tingaiwale mosavuta zimene tikukondwerera.
Pa Khirisimasi timaganiza za Mpulumutsi wathu. Koma kodi zimenezo zikutanthauzanji kwa ife?
Kodi mwaganizapo za Yesu, Mwana yekhayo wa Mulungu, ndi zimene Iye anachita kuti tikhale abale ndi alongo ake?
Kodi tikudziwa kuti nthawi zonse Mulungu ali pafupi kwambiri ndi ife? Tsiku lili lonse, m'moyo wathu wonse?
M'Baibulo, Yesu wapatsidwa mayina osiyanasiyana. Kodi munayamba mwaganizapo za zimene ena mwa mayina ndi maudindo amenewa amatanthauza kwa ife patokha?
Chikwangwani chimene ndinaona popita kuntchito chinandichititsa kuganizira za Khirisimasi yoyamba ku Betelehemu.