Kuti tiphunzire kwa Mbuye tiyenera kukhala osauka mumzimu.
Yesu anafotokoza kuti ndi njala ndi ludzu la chilungamo.