Pamene Yesu anadziitanira yekha kukadya chakudya ndi Zakeyu, wokhometsa msonkho, zinasintha moyo wa wokhometsa msonkho uja kwamuyaya.