Cholinga chomaliza m'moyo uno ndicho kukhala ndi mpumulo ndi mtendere m'mikhalidwe yonse, m'mavuto osiyanasiyana. Kodi timapeza bwanji mtendere wamtunduwu?