Chilichonse chinasintha pamene ndinamvetsa mtundu wa umunthu umene Yesu anali nawo pamene ankakhala padziko lapansi.
Baibulo limatiuza kuti "nthawi zonse khalani osangalala". Koma kodi zimenezi zingatheke bwanji?