Tikakhala ndi mzimu wa chikhulupiriro, Mulungu angatithandize kugonjetsa zinthu zimene zingaoneke ngati zosatheka.
Kodi anthufe tingatsatire bwanji Khristu, Mwana wa Mulungu?
Kodi kupachikidwa ndi nsembe za Yesu zinali zosiyana bwanji ndi nsembe ndi chikhululukiro m'Pangano Lakale?
Pamene ndilingalira za chiitano changa monga Mkristu, kodi ndili ndi chidwi chotani m'kuchikwaniritsa?
Nthawi zina "maluso" angatanthauze chinthu chosiyana kwambiri ndi zimene mungaganize.
Kodi ndingasunge bwanji moyo wanga woganiza kukhala woyera pamene ambiri mwa malingaliro awa angobwera popanda ine kuwafuna?
M'Baibulo, Yesu wapatsidwa mayina osiyanasiyana. Kodi munayamba mwaganizapo za zimene ena mwa mayina ndi maudindo amenewa amatanthauza kwa ife patokha?