Werengani nkhani yosonkhezera imeneyi yonena za kukhulupirika kwenikweni kwa Danieli, ndi chikhulupiriro chake mwa Mulungu zivute zitani.
Pali njira imodzi yokha yodziŵiradi Yesu.
N'chifukwa chiyani nthawi zonse mumakhala woyamikira komanso wosangalala, mosasamala kanthu za mmene zinthu zilili pa moyo wanu kapena mmene mukumvera.
Iye anali chabe mtsikana wabwinobwino wa ku Nazarete, koma anakhala mayi wa Yesu Kristu. Chifukwa chiyani iye?
Kodi ndimakhala ndi moyo kwa ndani? Kodi ndikutumikira Mulungu kapena anthu?