Zachokera m 'buku la Miyambo limanena kuti munthu wokhulupirika ndi wovuta kumupeza. Kodi ndinu mmodzi wa anthu ochepa amenewo?
Popeza sindingathe kugonjetsa uchimo popanda thandizo la Mzimu Woyera, n'kofunika kwambiri kuti ndimvetsere ndi kumvera pamene Mzimu akulankhula nane.