Tingakhale ndi mautumiki osiyanasiyana, koma tonsefe tingafike ku moyo womwewo monga wa atumwi.
Kodi tingakhale bwanji odzazidwa ndi ubwino wa Mulungu pamene mulibe chabwino mu umunthu wathu wokonda kuchita zoipa?
Yesu anaphunzitsa ophunzira Ake zimene zinali zofunika kwambiri kupempherera.