Maganizo odziona ngati wosafunika ndiponso oipa ponena za ine ankandilamulira, koma nditazindikira kuti zimenezi zinali uchimo, ndinapeza mphamvu zoti ndithane nazo.