Tikudziwa kuti Baibulo limanena kuti Mulungu amatikonda. Koma kodi Iye ali kuti m'nthaŵi zovuta?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kodi n'zotheka kudziwa Mulungu payekha?
Kodi mumakhulupirira zozizwitsa? Kodi chozizwitsa chimaoneka bwanji kwa inu?