Kodi "chigololo" n'chiyani mogwirizana ndi Mawu a Mulungu ndipo zotsatira za chigololo n'zotani?
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Pangakhale zifukwa zambiri zimene timayesedwera kuda nkhaŵa, koma tili ndi mphamvu yaikulu koposa m'chilengedwe chonse kumbali yathu!
Kodi ndingadziwe bwanji ngati "ndikukhala mabwenzi" ndi "dziko?"
Phunzirani zimene zidzachitike pa tsiku limene aliyense ayenera kuonekera pamaso pa Khristu kuti aweruzidwe
Ndikamayenda m'kuunika, moyo umakhala wabwino, ndipo nthawi zonse ndimakhala ndi chikumbumtima chabwino. Koma kodi ndimayenda bwanji m'kuunika?
Kumveka kwina pa nkhani yosangalatsa yomwe nthawi zambiri imamvedwa molakwika.
Timawerenga zambiri zokhudza mtima wa m'Baibulo. Koma kodi mtima wathu kwenikweni nchiyani, kunena mwauzimu? Kodi mtima wathu uli ndi kufunika kotani?
Pokhala ndi "chidziwitso" chochuluka chomwe chilipo ndipo aliyense akuyesera kutiuza kuti akunena zoona, kodi n'zotheka bwanji kudziwa zomwe zilidi zoona?
Kodi munayamba mwakayikirapo kuti Mulungu amakukondani? Mavesi a m'Baibulo amenewa angasinthe zimenezo.
Kukhulupirira si kungovomereza kuti Baibulo ndi loona.
M'Baibulo, Yesu wapatsidwa mayina osiyanasiyana. Kodi munayamba mwaganizapo za zimene ena mwa mayina ndi maudindo amenewa amatanthauza kwa ife patokha?