Mkhristu asanalandire Mzimu Woyera, mungamuyerekeze ndi galimoto yopanda injini.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Pa Pentekoste, ophunzirawo anabatizidwa ndi Mzimu Woyera ndi moto. Popanda moto umenewu sipangakhale mgwirizano.
Kodi mwakumana ndi mphamvu yodabwitsa yomwe imabwera mukadzazidwa ndi Mzimu?
Mwina imeneyi ndi imodzi mwa mavesi odziwika bwino a m'Baibulo okhudzana ndi Pentekoste, koma kodi cholinga cha mphamvu imeneyi n'chiyani?
Popeza sindingathe kugonjetsa uchimo popanda thandizo la Mzimu Woyera, n'kofunika kwambiri kuti ndimvetsere ndi kumvera pamene Mzimu akulankhula nane.
Kodi ndingayende bwanji mwa Mzimu?
Kodi Mzimu Woyera ndani? N'chifukwa chiyani ndimamufuna?