Kuchita chilungamo m'moyo wanga wa tsiku ndi tsiku ndiko kuchita zimene Mulungu akufuna kuti ndichite.
Moyo wa Chikirisitu Wochitachita
Kodi mwalingalira za chimene chilungamo chiridi ndi mphotho zake?
Yesu anafotokoza kuti ndi njala ndi ludzu la chilungamo.
Zimenezi n'zimene zimatanthauza kukhala Mkhristu amene amakonda kwambiri chikhulupiriro chawo.
Yesu ankatha kuona mmene Natanayeli analili asanalankhule ndi Iye. Kodi n'chiyani chinali chapadera kwambiri pa Natanayeli?
Pangakhale zifukwa zambiri za "kuchita chinthu choyenera". Kodi chifukwa chanu n'chiyani?
Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani ya ndalama?